2 Mafumu 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Ahazi anatumiza uthenga kwa Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri wakuti: “Ndine mtumiki wanu ndiponso mwana wanu. Bwerani mudzandipulumutse mʼmanja mwa mfumu ya Siriya ndi mʼmanja mwa mfumu ya Isiraeli, amene akundiukira.”
7 Choncho Ahazi anatumiza uthenga kwa Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri wakuti: “Ndine mtumiki wanu ndiponso mwana wanu. Bwerani mudzandipulumutse mʼmanja mwa mfumu ya Siriya ndi mʼmanja mwa mfumu ya Isiraeli, amene akundiukira.”