-
Yesaya 36:21, 22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma anthuwo anangokhala chete, osamuyankha chilichonse, chifukwa mfumu inawalamula kuti, “Musakamuyankhe.”+ 22 Ndiyeno Eliyakimu mwana wa Hilikiya amene ankayangʼanira banja lachifumu,* Sebina+ mlembi ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atangʼamba zovala zawo ndipo anamuuza zomwe Rabisake ananena.
-