Yesaya 38:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Yesaya anati: “Bweretsani keke ya nkhuyu zouma zoumba pamodzi ndipo muziike pachotupa chimene ali nacho kuti achire.”+ 22 Hezekiya anali atafunsa kuti: “Kodi chizindikiro chakuti ndidzapitadi kunyumba ya Yehova nʼchiyani?”+
21 Kenako Yesaya anati: “Bweretsani keke ya nkhuyu zouma zoumba pamodzi ndipo muziike pachotupa chimene ali nacho kuti achire.”+ 22 Hezekiya anali atafunsa kuti: “Kodi chizindikiro chakuti ndidzapitadi kunyumba ya Yehova nʼchiyani?”+