-
Ezekieli 8:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho anandipititsa kubwalo lamkati la nyumba ya Yehova.+ Ndiyeno ndinaona kuti pakhomo lolowera mʼkachisi wa Yehova, pakati pa khonde ndi guwa lansembe, panali amuna pafupifupi 25 atafulatira kachisi wa Yehova ndipo nkhope zawo zinali zitayangʼana kumʼmawa. Iwo ankagwadira dzuwa limene linali kumʼmawa.+
-