-
1 Mafumu 17:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Atamva zimenezi mayiyo anati: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wanu wamoyo, ndilibe mkate, koma ufa pangʼono mumtsuko waukulu ndi mafuta pangʼono mumtsuko waungʼono.+ Panopa ndikutola tinkhuni kuti ndipite kukaphika chakudya choti ineyo ndi mwana wanga tidye. Tikadya, tiziyembekezera kufa.”
-