2 Mafumu 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu amene anawasiya ku Yuda.+ Yeremiya 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Ahikamu,+ mwana wa Safani+ anateteza Yeremiya, nʼchifukwa chake sanaperekedwe kwa anthu kuti amuphe.+
22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu amene anawasiya ku Yuda.+
24 Koma Ahikamu,+ mwana wa Safani+ anateteza Yeremiya, nʼchifukwa chake sanaperekedwe kwa anthu kuti amuphe.+