Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musakhale ndi milungu ina iliyonse kupatulapo ine.*+ Deuteronomo 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo ankapereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sankaidziwa,Kwa milungu yatsopano yongobwera kumene,Komanso kwa milungu imene makolo anu sankaidziwa. Oweruza 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa mʼdziko la Iguputo+ nʼkuyamba kutsatira milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milunguyo ndipo anakhumudwitsa Yehova.+ Yeremiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi pali mtundu uliwonse wa anthu umene unasinthapo milungu yawo nʼkuyamba kulambira milungu imene kulibeko? Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zopanda phindu.+
17 Iwo ankapereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sankaidziwa,Kwa milungu yatsopano yongobwera kumene,Komanso kwa milungu imene makolo anu sankaidziwa.
12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa mʼdziko la Iguputo+ nʼkuyamba kutsatira milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milunguyo ndipo anakhumudwitsa Yehova.+
11 Kodi pali mtundu uliwonse wa anthu umene unasinthapo milungu yawo nʼkuyamba kulambira milungu imene kulibeko? Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zopanda phindu.+