Yoswa 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuchokera mʼfuko la Benjamini, anawapatsa Gibiyoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba ndi malo ake odyetserako ziweto,+ Yoswa 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mizinda yonse imene anapereka kwa ansembe, ana a Aroni, inalipo 13 ndi malo ake odyetserako ziweto.+ 1 Mafumu 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Mfumu Asa inaitanitsa Ayuda onse moti palibe amene anatsala, ndipo iwo anatenga miyala ndi matabwa za ku Rama zimene Basa ankamangira. Mfumu Asa anatenga zinthu zimenezi nʼkukamangira mzinda wa Geba+ ku Benjamini ndi wa Mizipa+ kuti mizindayi ikhale yolimba.
17 Kuchokera mʼfuko la Benjamini, anawapatsa Gibiyoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba ndi malo ake odyetserako ziweto,+
19 Mizinda yonse imene anapereka kwa ansembe, ana a Aroni, inalipo 13 ndi malo ake odyetserako ziweto.+
22 Ndiyeno Mfumu Asa inaitanitsa Ayuda onse moti palibe amene anatsala, ndipo iwo anatenga miyala ndi matabwa za ku Rama zimene Basa ankamangira. Mfumu Asa anatenga zinthu zimenezi nʼkukamangira mzinda wa Geba+ ku Benjamini ndi wa Mizipa+ kuti mizindayi ikhale yolimba.