Deuteronomo 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi kumalo amenewo pamaso pa Yehova Mulungu wanu,+ ndipo muzidzasangalala ndi zochita zanu zonse+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani. 2 Mbiri 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa tsiku la 23 la mwezi wa 7, Solomo anauza anthuwo kuti azipita kwawo. Iwo anapita akusangalala+ komanso akumva bwino mumtima, chifukwa cha zabwino zimene Yehova anachitira Davide, Solomo ndiponso anthu ake Aisiraeli.+ Nehemiya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya ndiponso kukasangalala kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+
7 Inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi kumalo amenewo pamaso pa Yehova Mulungu wanu,+ ndipo muzidzasangalala ndi zochita zanu zonse+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.
10 Pa tsiku la 23 la mwezi wa 7, Solomo anauza anthuwo kuti azipita kwawo. Iwo anapita akusangalala+ komanso akumva bwino mumtima, chifukwa cha zabwino zimene Yehova anachitira Davide, Solomo ndiponso anthu ake Aisiraeli.+
12 Ndiyeno anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya ndiponso kukasangalala kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+