2 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana atatu aamuna a Zeruya,+ omwe ndi Yowabu,+ Abisai+ ndi Asaheli+ analinso pompo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala. 2 Samueli 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho Yowabu ndi mchimwene wake Abisai+ anapha Abineri+ chifukwa chakuti iye anapha Asaheli mchimwene wawo pa nkhondo+ ku Gibiyoni. 2 Samueli 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Asaheli+ mchimwene wake wa Yowabu anali mʼgulu la amuna 30 aja. Mʼgululi munalinso Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,+
18 Ana atatu aamuna a Zeruya,+ omwe ndi Yowabu,+ Abisai+ ndi Asaheli+ analinso pompo. Asaheli anali waliwiro kwambiri ngati mbawala.
30 Choncho Yowabu ndi mchimwene wake Abisai+ anapha Abineri+ chifukwa chakuti iye anapha Asaheli mchimwene wawo pa nkhondo+ ku Gibiyoni.
24 Asaheli+ mchimwene wake wa Yowabu anali mʼgulu la amuna 30 aja. Mʼgululi munalinso Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,+