-
2 Samueli 13:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Kenako Abisalomu analamula atumiki ake kuti: “Mukhale tcheru ndipo Aminoni akangofika posangalala ndi vinyo, ine ndikuuzani kuti, ‘Mupheni Aminoni!’ Zikatero mumuphe. Musaope. Ine ndi amene ndakulamulani. Muchite zinthu mwamphamvu komanso molimba mtima.”
-