Mateyu 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Iwe Betelehemu wamʼdziko la Yuda, si iwe mzinda waungʼono kwambiri kwa olamulira a Yuda, chifukwa mwa iwe mudzatuluka wolamulira amene azidzaweta anthu anga, Aisiraeli.’”+ Aheberi 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anachokera ku fuko la Yuda+ koma Mose sananenepo kuti ansembe adzachokera mu fuko limeneli.
6 ‘Iwe Betelehemu wamʼdziko la Yuda, si iwe mzinda waungʼono kwambiri kwa olamulira a Yuda, chifukwa mwa iwe mudzatuluka wolamulira amene azidzaweta anthu anga, Aisiraeli.’”+
14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anachokera ku fuko la Yuda+ koma Mose sananenepo kuti ansembe adzachokera mu fuko limeneli.