Oweruza 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu a fuko la Benjamini sanathamangitse Ayebusi a ku Yerusalemu, moti Ayebusiwo akukhalabe ndi anthu a fuko la Benjamini ku Yerusalemu mpaka lero.+
21 Anthu a fuko la Benjamini sanathamangitse Ayebusi a ku Yerusalemu, moti Ayebusiwo akukhalabe ndi anthu a fuko la Benjamini ku Yerusalemu mpaka lero.+