1 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso Aisiraeli anatenga mizinda imene Afilisitiwo analanda kuyambira ku Ekironi mpaka ku Gati. Kuwonjezera pamenepo, Aisiraeli anatenganso dera lawo lomwe Afilisiti anawalanda. Komanso pakati pa Aisiraeli ndi Aamori panali mtendere.+ 1 Samueli 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi,* dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali pafupifupi mamita atatu.*
14 Komanso Aisiraeli anatenga mizinda imene Afilisitiwo analanda kuyambira ku Ekironi mpaka ku Gati. Kuwonjezera pamenepo, Aisiraeli anatenganso dera lawo lomwe Afilisiti anawalanda. Komanso pakati pa Aisiraeli ndi Aamori panali mtendere.+
4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi,* dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali pafupifupi mamita atatu.*