-
Nehemiya 11:7-9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Anthu a fuko la Benjamini anali awa: Salelu+ mwana wa Mesulamu, Mesulamu anali mwana wa Yoedi, Yoedi anali mwana wa Pedaya, Pedaya anali mwana wa Kolaya, Kolaya anali mwana wa Maaseya, Maaseya anali mwana wa Itiyeli ndipo Itiyeli anali mwana wa Yesaiya. 8 Pambuyo pa Salelu panali Gabai ndi Salai ndipo onse pamodzi analipo 928. 9 Yoweli mwana wa Zikiri anali woyangʼanira wawo ndipo Yuda mwana wa Hasenuwa anali wachiwiri kwa woyangʼanira mzinda.
-