Ekisodo 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo Eleazara+ mwana wa Aroni, anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anamʼberekera Pinihasi.+ Amenewa ndi atsogoleri a mabanja amʼfuko la Levi, mogwirizana ndi mabanja awo.+ Numeri 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndi amene ankayangʼanira anthu onse amene ankatumikira pamalo oyera.
25 Ndipo Eleazara+ mwana wa Aroni, anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anamʼberekera Pinihasi.+ Amenewa ndi atsogoleri a mabanja amʼfuko la Levi, mogwirizana ndi mabanja awo.+
32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndi amene ankayangʼanira anthu onse amene ankatumikira pamalo oyera.