-
1 Samueli 26:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma Davide anauza Abisai kuti: “Ayi, usamubaye. Ndani angavulaze wodzozedwa wa Yehova+ nʼkukhala wopanda mlandu?”+ 10 Davide anapitiriza kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova, Mulungu wamoyo, Yehova adzamulanga yekha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira, kapenanso adzapita kunkhondo nʼkukaphedwa.+
-