Oweruza 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Afilisiti anamʼgwira ndipo anamuboola maso. Kenako anapita naye ku Gaza nʼkumumanga ndi matcheni awiri akopa,* ndipo iye ankayendetsa mwala wa mphero mʼndende. Oweruza 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Olamulira a Afilisiti anasonkhana kuti apereke nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo komanso kuti achite chikondwerero, popeza ankanena kuti: “Mulungu wathu watipatsa mdani wathu Samisoni!”
21 Choncho Afilisiti anamʼgwira ndipo anamuboola maso. Kenako anapita naye ku Gaza nʼkumumanga ndi matcheni awiri akopa,* ndipo iye ankayendetsa mwala wa mphero mʼndende.
23 Olamulira a Afilisiti anasonkhana kuti apereke nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo komanso kuti achite chikondwerero, popeza ankanena kuti: “Mulungu wathu watipatsa mdani wathu Samisoni!”