12 Choncho Davide anapita kukatenga mafupa a Sauli ndi mafupa a Yonatani mwana wake kwa atsogoleri a ku Yabesi-giliyadi.+ Atsogoleriwo anakatenga mobisa mtembo wa Sauli ndi wa Yonatani mʼbwalo la mzinda wa Beti-sani, kumene Afilisiti anaipachika, tsiku limene anapha Sauli paphiri la Giliboa.+