27 Pamene Samueli ankatembenuka kuti azipita, Sauli anagwira mʼmunsi mwa mkanjo wodula manja wa Samueli ndipo mkanjowo unangʼambika. 28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wangʼamba ufumu wa Isiraeli nʼkuuchotsa kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa munthu wina woyenera kuposa iweyo.+