2 Atatero, Davide anagawa anthuwo mʼmagulu atatu. Gulu loyamba analipereka kwa Yowabu,+ gulu lachiwiri analipereka kwa Abisai+ mwana wa Zeruya,+ mchimwene wake wa Yowabu, ndipo gulu lachitatu analipereka kwa Itai+ wa ku Gati. Kenako mfumu inauza anthuwo kuti: “Inenso ndipita nanu.”