Yesaya 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova adzaimirira ngati mmene anachitira paphiri la Perazimu.Adzaimirira ngati mmene anachitira mʼchigwa, pafupi ndi Gibiyoni,+Kuti achite zochita zake, zochita zake zodabwitsa,Komanso kuti agwire ntchito yake, ntchito yake yachilendo.+
21 Yehova adzaimirira ngati mmene anachitira paphiri la Perazimu.Adzaimirira ngati mmene anachitira mʼchigwa, pafupi ndi Gibiyoni,+Kuti achite zochita zake, zochita zake zodabwitsa,Komanso kuti agwire ntchito yake, ntchito yake yachilendo.+