25 Davide ndi atsogoleri a magulu a anthu otumikira, anasankha ena mwa ana a Asafu, a Hemani ndi a Yedutuni+ kuti azitumikira polosera ndi azeze, zoimbira za zingwe+ ndi zinganga.+ Anthu audindo amene anawasankha kuti azichita utumiki umenewu anali awa: