-
2 Samueli 7:1-3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mfumu inkakhala mʼnyumba yake*+ ndipo Yehova anachititsa kuti izikhala mwamtendere komanso isamavutitsidwe ndi adani ake onse. 2 Ndiyeno mfumuyo inauza mneneri Natani+ kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene Likasa la Mulungu woona likukhala mutenti.”+ 3 Natani anauza mfumu kuti: “Chitani chilichonse chimene mtima wanu ukufuna, chifukwa Yehova ali nanu.”+
-