21 Zitatero Mose anavomereza kukhala ndi Reueli, ndipo iye anapereka Zipora+ mwana wake wamkazi kwa Mose kuti akhale mkazi wake. 22 Kenako Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anamʼpatsa dzina lakuti Gerisomu,+ chifukwa anati, “Ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.”+