2 Mafumu 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Hezekiya atamva zimenezi anauza Yesaya kuti: “Mawu a Yehova amene mwanenawa ndi abwino.”+ Anapitiriza kuti: “Ngati mʼmasiku anga mukhale bata ndi mtendere, ndiye kuti zili bwino.”+
19 Hezekiya atamva zimenezi anauza Yesaya kuti: “Mawu a Yehova amene mwanenawa ndi abwino.”+ Anapitiriza kuti: “Ngati mʼmasiku anga mukhale bata ndi mtendere, ndiye kuti zili bwino.”+