-
Ekisodo 38:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kenako anapanga ziwiya zonse zogwiritsa ntchito paguwalo. Anapanga ndowa, mafosholo, mbale zolowa, mafoloko aakulu ndi zopalira moto. Ziwiya zake zonse anazipanga ndi kopa.
-