1 Mafumu 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anamanga bwalo lamkati+ la mizere itatu ya miyala yosema komanso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.+ 1 Mafumu 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwalo lalikulu linazunguliridwa ndi khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu kuchokera pansi ndi mzere umodzi wa matabwa a mkungudza pamwamba pake. Ndi mmenenso zinalili ndi bwalo lamkati+ la nyumba ya Yehova komanso khonde la nyumbayo.+
36 Anamanga bwalo lamkati+ la mizere itatu ya miyala yosema komanso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.+
12 Bwalo lalikulu linazunguliridwa ndi khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu kuchokera pansi ndi mzere umodzi wa matabwa a mkungudza pamwamba pake. Ndi mmenenso zinalili ndi bwalo lamkati+ la nyumba ya Yehova komanso khonde la nyumbayo.+