2 Mbiri 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atatero anapita kumene kunali Mfumu Hezekiya nʼkukaiuza kuti: “Tayeretsa nyumba yonse ya Yehova, guwa lansembe zopsereza+ ndi ziwiya zake zonse.+ Tayeretsanso tebulo loikapo mkate wosanjikiza*+ ndi ziwiya zake zonse.
18 Atatero anapita kumene kunali Mfumu Hezekiya nʼkukaiuza kuti: “Tayeretsa nyumba yonse ya Yehova, guwa lansembe zopsereza+ ndi ziwiya zake zonse.+ Tayeretsanso tebulo loikapo mkate wosanjikiza*+ ndi ziwiya zake zonse.