2 Mbiri 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Alevi omwe anali mbadwa za Kohati+ ndi za Kora anaimirira nʼkuyamba kutamanda Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mawu okweza kwambiri.+
19 Kenako Alevi omwe anali mbadwa za Kohati+ ndi za Kora anaimirira nʼkuyamba kutamanda Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mawu okweza kwambiri.+