2 Mafumu 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu amene anawasiya ku Yuda.+ Yeremiya 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya a Amoni,+ watumiza Isimaeli mwana wa Netaniya kuti adzakuphe?”+ Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanawakhulupirire.
22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu amene anawasiya ku Yuda.+
14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya a Amoni,+ watumiza Isimaeli mwana wa Netaniya kuti adzakuphe?”+ Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanawakhulupirire.