Deuteronomo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova adzakutumizirani matemberero, chisokonezo ndi chilango pa chilichonse chimene mukuchita mpaka mutawonongedwa nʼkutha mofulumira, chifukwa cha zinthu zoipa zimene mukuchita komanso chifukwa choti mwandisiya.+
20 Yehova adzakutumizirani matemberero, chisokonezo ndi chilango pa chilichonse chimene mukuchita mpaka mutawonongedwa nʼkutha mofulumira, chifukwa cha zinthu zoipa zimene mukuchita komanso chifukwa choti mwandisiya.+