2 Mafumu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova anayamba kumʼtumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu ndi a Aamoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene ananena kudzera mwa atumiki ake, aneneri.
2 Yehova anayamba kumʼtumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu ndi a Aamoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene ananena kudzera mwa atumiki ake, aneneri.