Maliro 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anyamata ndi amuna okalamba afa ndipo mitembo yawo ili pansi mʼmisewu.+ Anamwali* anga ndi anyamata anga aphedwa ndi lupanga.+ Mwawapha pa tsiku la mkwiyo wanu. Mwawapha mopanda chisoni.+
21 Anyamata ndi amuna okalamba afa ndipo mitembo yawo ili pansi mʼmisewu.+ Anamwali* anga ndi anyamata anga aphedwa ndi lupanga.+ Mwawapha pa tsiku la mkwiyo wanu. Mwawapha mopanda chisoni.+