1 Mbiri 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Davide anauza atsogoleri a Alevi kuti asankhe abale awo oimba kuti aimbe mosangalala komanso agwiritse ntchito zipangizo zoimbira. Zipangizozo zinali zoimbira za zingwe, azeze+ ndi zinganga.+
16 Kenako Davide anauza atsogoleri a Alevi kuti asankhe abale awo oimba kuti aimbe mosangalala komanso agwiritse ntchito zipangizo zoimbira. Zipangizozo zinali zoimbira za zingwe, azeze+ ndi zinganga.+