1 Mbiri 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Awa ndi anthu amene Davide anawapatsa udindo wotsogolera kuimba panyumba ya Yehova ataikapo Likasa.+ 1 Mbiri 6:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mʼbale wake Asafu+ ankaima kumanja kwake. Asafu anali mwana wa Berekiya, Berekiya anali mwana wa Simeya,
31 Awa ndi anthu amene Davide anawapatsa udindo wotsogolera kuimba panyumba ya Yehova ataikapo Likasa.+
39 Mʼbale wake Asafu+ ankaima kumanja kwake. Asafu anali mwana wa Berekiya, Berekiya anali mwana wa Simeya,