Deuteronomo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iye asakhale ndi mahatchi ambiri+ kapena kuchititsa anthu kuti abwerere ku Iguputo kuti akatenge mahatchi ochuluka+ chifukwa Yehova anakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’ 1 Mafumu 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Solomo anali ndi makola 4,000* a mahatchi okoka magaleta ake komanso mahatchi* 12,000.+
16 Koma iye asakhale ndi mahatchi ambiri+ kapena kuchititsa anthu kuti abwerere ku Iguputo kuti akatenge mahatchi ochuluka+ chifukwa Yehova anakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’