Salimo 130:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Ya,* mukanakhala kuti mumayangʼanitsitsa* zolakwa,Ndi ndani akanaima pamaso panu, inu Yehova?+ Mlaliki 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa padziko lapansi palibe munthu wolungama amene amachita zabwino nthawi zonse ndipo sachimwa.+ Aroma 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Popeza anthu onse ndi ochimwa ndipo amalephera kusonyeza bwinobwino ulemerero wa Mulungu.+
20 Chifukwa padziko lapansi palibe munthu wolungama amene amachita zabwino nthawi zonse ndipo sachimwa.+