2 Kenako Mfumu Davide anaimirira nʼkunena kuti:
“Ndimvereni inu abale anga ndi anthu anga. Ineyo ndinafunitsitsa kumanga nyumba yoti likasa la pangano la Yehova lizikhalamo ndiponso yoti ikhale ngati chopondapo mapazi cha Mulungu wathu+ ndipo ndinakonzekera kuti ndiimange.+