Machitidwe 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo mfundo yakuti iye anamuukitsa ndipo sangabwererenso kuthupi limene limavunda,* anaifotokoza chonchi: ‘Ine ndidzakusonyezani anthu inu chikondi chokhulupirika chimene ndinalonjeza Davide. Lonjezo limeneli ndi lodalirika.’+
34 Ndipo mfundo yakuti iye anamuukitsa ndipo sangabwererenso kuthupi limene limavunda,* anaifotokoza chonchi: ‘Ine ndidzakusonyezani anthu inu chikondi chokhulupirika chimene ndinalonjeza Davide. Lonjezo limeneli ndi lodalirika.’+