1 Mafumu 8:62, 63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Kenako mfumu ndi Aisiraeli onsewo anayamba kupereka nsembe zambiri kwa Yehova.+ 63 Solomo anapereka nsembe zamgwirizano+ kwa Yehova. Anapereka ngʼombe 22,000 ndi nkhosa 120,000. Choncho mfumuyo ndi Aisiraeli onse anatsegulira nyumba ya Yehova.+
62 Kenako mfumu ndi Aisiraeli onsewo anayamba kupereka nsembe zambiri kwa Yehova.+ 63 Solomo anapereka nsembe zamgwirizano+ kwa Yehova. Anapereka ngʼombe 22,000 ndi nkhosa 120,000. Choncho mfumuyo ndi Aisiraeli onse anatsegulira nyumba ya Yehova.+