Yesaya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo,Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga. Yeremiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi pali mtundu uliwonse wa anthu umene unasinthapo milungu yawo nʼkuyamba kulambira milungu imene kulibeko? Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zopanda phindu.+
8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo,Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.
11 Kodi pali mtundu uliwonse wa anthu umene unasinthapo milungu yawo nʼkuyamba kulambira milungu imene kulibeko? Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zopanda phindu.+