1 Mafumu 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khomo lolowera kuchipinda chamʼmbali chapansi linali kumʼmwera* kwa nyumbayo,+ ndipo ankakwera masitepe oyenda mokhotakhota kukafika kuchipinda chapakati, kenako kukafika kuchipinda chachitatu.
8 Khomo lolowera kuchipinda chamʼmbali chapansi linali kumʼmwera* kwa nyumbayo,+ ndipo ankakwera masitepe oyenda mokhotakhota kukafika kuchipinda chapakati, kenako kukafika kuchipinda chachitatu.