1 Mafumu 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Panalinso Yerobowamu,+ mwana wa Nebati, wa fuko la Efuraimu, wa ku Zereda. Iye anali mtumiki wa Solomo.+ Mayi ake anali mkazi wamasiye dzina lake Zeruwa. Nayenso Yerobowamu anayamba kuukira mfumu.+
26 Panalinso Yerobowamu,+ mwana wa Nebati, wa fuko la Efuraimu, wa ku Zereda. Iye anali mtumiki wa Solomo.+ Mayi ake anali mkazi wamasiye dzina lake Zeruwa. Nayenso Yerobowamu anayamba kuukira mfumu.+