Oweruza 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Ndidzakupulumutsani pogwiritsa ntchito amuna 300 amene amwa madzi ndi manja awo, ndipo ndidzapereka Amidiyani mʼmanja mwanu.+ Koma ena onsewo abwerere kunyumba.” 1 Samueli 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yonatani anauza womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tipite kwa amuna osadulidwawa.+ Mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+
7 Ndiyeno Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Ndidzakupulumutsani pogwiritsa ntchito amuna 300 amene amwa madzi ndi manja awo, ndipo ndidzapereka Amidiyani mʼmanja mwanu.+ Koma ena onsewo abwerere kunyumba.”
6 Choncho Yonatani anauza womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tipite kwa amuna osadulidwawa.+ Mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+