-
Yeremiya 23:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, azinena zoona polankhula mawu angawo.”
“Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?” akutero Yehova.
-