-
Deuteronomo 4:29-31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mukadzamufunafuna ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse, mudzamupezadi.+ 30 Pamapeto pake, zinthu zonsezi zikadzakuchitikirani nʼkukhala pamavuto aakulu, mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndipo mudzamvera mawu ake.+ 31 Pajatu Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakusiyani kapena kukuwonongani kapenanso kuiwala pangano limene analumbira kwa makolo anu.+
-