2 Mbiri 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anatulutsa mwana wa mfumu+ uja nʼkumuveka chipewa chachifumu nʼkuika mpukutu wa Chilamulo+ cha Mulungu pamutu pake. Choncho anthuwo anamuveka ufumu ndipo Yehoyada ndi ana ake anamudzoza. Kenako anati: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+
11 Kenako anatulutsa mwana wa mfumu+ uja nʼkumuveka chipewa chachifumu nʼkuika mpukutu wa Chilamulo+ cha Mulungu pamutu pake. Choncho anthuwo anamuveka ufumu ndipo Yehoyada ndi ana ake anamudzoza. Kenako anati: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”+