Yesaya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Masomphenya amene Yesaya*+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+ Hoseya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Yehova analankhula ndi Hoseya* mwana wa Beeri mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda,+ ndiponso mʼmasiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli. Mateyu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hezekiya anabereka Manase.+Manase anabereka Amoni.+Amoni anabereka Yosiya.+
1 Masomphenya amene Yesaya*+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+
1 Yehova analankhula ndi Hoseya* mwana wa Beeri mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda,+ ndiponso mʼmasiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli.