-
2 Mafumu 6:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma iye anati: “Usaope,+ ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi iwowo.”+ 17 Kenako Elisa anayamba kupemphera kuti: “Inu Yehova, chonde mutseguleni maso kuti aone.”+ Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso a mtumikiyo, moti anaona kuti dera lonse lamapiri kuzungulira Elisa+ linadzaza ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo oyaka moto.+
-